Jump to content

Tsamba Lalikulu

From Wikipedia

Mwalandilidwa pa Wikipedia,
encyclopedia yaulere imene aliyense angathandizile kukuza!
Pakali pano tili ndi nkhani zokwana 1,066 mu chiChewa, chinenero chomwe chimayankhulidwa ku Malawi ndi Zambia.

Chithunzi cha tsikulo

Mawu akuti Kukana Petro' amatanthauza kukana katatu kwa Yesu kochitidwa ndi Mtumwi Petro, monga momwe Baibulo limafotokozera. [Mauthenga Abwino] onse anayi a m’Chipangano Chatsopano Chipangano Chatsopano amanena kuti mkati mwa Mgonero Womaliza ndi ophunzira ake, iye analosera kuti Petro akakana za iye tambala asanalire m’maŵa mwake. Malinga ndi nkhaniyo, ulosiwu unakwaniritsidwa pambuyo pa kumangidwa kwa Yesu, Petulo anakana katatu kuti sakumudziwa. Atamukana kachitatu, Petulo anamva tambala akulira ndipo anakumbukira zimene analoserazo, zomwe zinachititsa kuti alire momvetsa chisoni.

Chithunzichi ndi chojambula chamafuta pansalu chojambulidwa ndi Gerard Seghers, chosonyeza Kukana kwa Petro. Idayamba cha m'ma 1620-1625 ndipo tsopano ikugwiridwa ndi North Carolina Museum of Art.

Kujambula ndi: Gerard Seghers

Wikipedia Muzinenero Zina

Ntchito zina za Wikimedia

Wikipedia imayang'aniridwa ndi Wikimedia Foundation, bungwe lopanda phindu lomwe limakhalanso ndi mapulojekiti:
Commons
Malo omwe aliyense angapeze ndikugawana zithunzi, makanema, ndi mawu aulere.
Wikifunctions
Malo omwe mungapeze ndikugwiritsa ntchito zida zothandiza ndi njira zazifupi pantchito zosiyanasiyana.
Wikidata
Malo omwe chidziwitso chimakonzedwa ndikusungidwa m'njira yoti aliyense azitha kuzipeza ndikuzigwiritsa ntchito momasuka.
Wikispecies
Mndandanda wa nyama zosiyanasiyana, zomera, ndi zamoyo zina.
Wikipedia
Buku lalikulu lapaintaneti lodzaza ndi zambiri zolembedwa mchingerezi zomwe aliyense angaziwerenge ndikuwongolera.
Wikiquote
Malo omwe mungapezeko mawu otchuka komanso osangalatsa ochokera kwa anthu.
Wikinews
Nkhani zomwe aliyense angathe kuziwerenga, kugawana, ndi kuthandiza kulemba.
Wiktionary
Dictionary and thesaurus
Wikiversity
Zida zaulere monga mabuku, makanema, ndi maupangiri omwe amakuthandizani kuphunzira zinthu zatsopano.
Wikibooks
Malo omwe mungapeze mabuku ndi malangizo okuthandizani kuphunzira, ndipo ndi omasuka kugwiritsa ntchito.
Wikisource
Laibulale komwe mungapeze mabuku, zithunzi, ndi zinthu zina zaulere kuti aliyense azigwiritsa ntchito.
MediaWiki
Malo omwe anthu amagwira ntchito popanga ndi kukonza mapulogalamu omwe amayendetsa Wikipedia ndi mawebusayiti ena a Wiki.
Meta-Wiki
Malo oti anthu ogwira ntchito pa Wikipedia ndi ma projekiti ena akonzekere, kukonza, ndi kugwirira ntchito limodzi.
Wikivoyage
Upangiri waulere womwe umakuthandizani kuti muphunzire za malo omwe mungayendere, zinthu zoti muchite, komanso momwe mungayendere.


Purge server cache